×

Iye adalenga kumwamba ndi dziko lapansi m’choonadi Iye amapanga usiku kuti uphimbe 39:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:5) ayat 5 in Chichewa

39:5 Surah Az-Zumar ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 5 - الزُّمَر - Page - Juz 23

﴿خَلَقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ بِٱلۡحَقِّۖ يُكَوِّرُ ٱلَّيۡلَ عَلَى ٱلنَّهَارِ وَيُكَوِّرُ ٱلنَّهَارَ عَلَى ٱلَّيۡلِۖ وَسَخَّرَ ٱلشَّمۡسَ وَٱلۡقَمَرَۖ كُلّٞ يَجۡرِي لِأَجَلٖ مُّسَمًّىۗ أَلَا هُوَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡغَفَّٰرُ ﴾
[الزُّمَر: 5]

Iye adalenga kumwamba ndi dziko lapansi m’choonadi Iye amapanga usiku kuti uphimbe usana ndiponso amapanga usana kuti uphimbe usiku ndipo adalamula dzuwa ndi mwezi kukhala zopanda mphamvu. Chilichonse kumaenda mu msewu wakewake. Ndithudi Iye ndi wamphamvu, ndi wokhululukira nthawi zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: خلق السموات والأرض بالحق يكور الليل على النهار ويكور النهار على الليل, باللغة نيانجا

﴿خلق السموات والأرض بالحق يكور الليل على النهار ويكور النهار على الليل﴾ [الزُّمَر: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Adalenga thambo ndi nthaka mwamtheradi. Amakulunga usiku mu usana; ndipo amakulunga usana mu usiku. Ndipo dzuwa ndi mwezi wazichita kuti zitumikire monga momwe afunira. Zonsezi zikuyenda kufikira pa nthawi yake imene yaikidwa. Dziwani kuti Iye (Allah) Ngwamphamvu zoposa; Ngokhululuka kwambiri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek