×

Lapani kwa Ambuye wanu nthawi ndi nthawi ndipo mudzipereke kwathunthu kwa Iye 39:54 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:54) ayat 54 in Chichewa

39:54 Surah Az-Zumar ayat 54 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 54 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿وَأَنِيبُوٓاْ إِلَىٰ رَبِّكُمۡ وَأَسۡلِمُواْ لَهُۥ مِن قَبۡلِ أَن يَأۡتِيَكُمُ ٱلۡعَذَابُ ثُمَّ لَا تُنصَرُونَ ﴾
[الزُّمَر: 54]

Lapani kwa Ambuye wanu nthawi ndi nthawi ndipo mudzipereke kwathunthu kwa Iye chilango chisanadze kwa inu chifukwa sipadzakhala wina wothandiza inu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأنيبوا إلى ربكم وأسلموا له من قبل أن يأتيكم العذاب ثم لا, باللغة نيانجا

﴿وأنيبوا إلى ربكم وأسلموا له من قبل أن يأتيكم العذاب ثم لا﴾ [الزُّمَر: 54]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tembenukirani kwa Mbuye wanu, ndipo m’gonjereni chilango chisadakudzereni. Ndipo zitatero, sim’dzapulumutsidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek