×

Ndipo pamene inu muyenda padziko lapansi sikulakwa kwa inu kupungula mapemphero ngati 4:101 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:101) ayat 101 in Chichewa

4:101 Surah An-Nisa’ ayat 101 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 101 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَإِذَا ضَرَبۡتُمۡ فِي ٱلۡأَرۡضِ فَلَيۡسَ عَلَيۡكُمۡ جُنَاحٌ أَن تَقۡصُرُواْ مِنَ ٱلصَّلَوٰةِ إِنۡ خِفۡتُمۡ أَن يَفۡتِنَكُمُ ٱلَّذِينَ كَفَرُوٓاْۚ إِنَّ ٱلۡكَٰفِرِينَ كَانُواْ لَكُمۡ عَدُوّٗا مُّبِينٗا ﴾
[النِّسَاء: 101]

Ndipo pamene inu muyenda padziko lapansi sikulakwa kwa inu kupungula mapemphero ngati muopa kuti anthu osakhulupirira akuvutitsani. Ndithudi anthu osakhulupirira ndi adani anu enieni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا ضربتم في الأرض فليس عليكم جناح أن تقصروا من الصلاة إن, باللغة نيانجا

﴿وإذا ضربتم في الأرض فليس عليكم جناح أن تقصروا من الصلاة إن﴾ [النِّسَاء: 101]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati mukuyenda pa dziko, sikulakwa kwa inu kufupikitsa Swala ngati mukuopa kuti angakusokonezeni omwe sadakhulupirire. Ndithudi, osakhulupirira ndi adani anu oonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek