×

Ndipo ngati mkazi aopa kuzunzidwa kapena kusiyidwa ndi mwamuna wake, sichidzakhala chinthu 4:128 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:128) ayat 128 in Chichewa

4:128 Surah An-Nisa’ ayat 128 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 128 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَإِنِ ٱمۡرَأَةٌ خَافَتۡ مِنۢ بَعۡلِهَا نُشُوزًا أَوۡ إِعۡرَاضٗا فَلَا جُنَاحَ عَلَيۡهِمَآ أَن يُصۡلِحَا بَيۡنَهُمَا صُلۡحٗاۚ وَٱلصُّلۡحُ خَيۡرٞۗ وَأُحۡضِرَتِ ٱلۡأَنفُسُ ٱلشُّحَّۚ وَإِن تُحۡسِنُواْ وَتَتَّقُواْ فَإِنَّ ٱللَّهَ كَانَ بِمَا تَعۡمَلُونَ خَبِيرٗا ﴾
[النِّسَاء: 128]

Ndipo ngati mkazi aopa kuzunzidwa kapena kusiyidwa ndi mwamuna wake, sichidzakhala chinthu cholakwa kwa iwo awiriwo ngati onse afuna kugwirizana pakati pawo chifukwa mgwirizano ndi wabwino. Ndipo umunthu umalamulidwa ndi umbombo. Koma ngati inu muchita chinthu chabwino ndi kulewa zoipa, ndithudi Mulungu amadziwa zonse zimene mukuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن امرأة خافت من بعلها نشوزا أو إعراضا فلا جناح عليهما أن, باللغة نيانجا

﴿وإن امرأة خافت من بعلها نشوزا أو إعراضا فلا جناح عليهما أن﴾ [النِّسَاء: 128]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek