Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 152 - النِّسَاء - Page - Juz 6
﴿وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ بِٱللَّهِ وَرُسُلِهِۦ وَلَمۡ يُفَرِّقُواْ بَيۡنَ أَحَدٖ مِّنۡهُمۡ أُوْلَٰٓئِكَ سَوۡفَ يُؤۡتِيهِمۡ أُجُورَهُمۡۚ وَكَانَ ٱللَّهُ غَفُورٗا رَّحِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 152]
﴿والذين آمنوا بالله ورسله ولم يفرقوا بين أحد منهم أولئك سوف يؤتيهم﴾ [النِّسَاء: 152]
Khaled Ibrahim Betala “Tsopano amene akhulupirira Allah ndi atumiki Ake, napanda kulekanitsa pakati pa aliyense wa iwo (koma nkuwakhulupirira onse), iwo adzawapatsa malipiro awo. Ndipo Allah Ngokhululuka kwambiri, Wachisoni chosatha |