×

Apatseni ana a masiye chuma chawo akafika msinkhu woyenera. Musasinthitse choipa ndi 4:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:2) ayat 2 in Chichewa

4:2 Surah An-Nisa’ ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 2 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿وَءَاتُواْ ٱلۡيَتَٰمَىٰٓ أَمۡوَٰلَهُمۡۖ وَلَا تَتَبَدَّلُواْ ٱلۡخَبِيثَ بِٱلطَّيِّبِۖ وَلَا تَأۡكُلُوٓاْ أَمۡوَٰلَهُمۡ إِلَىٰٓ أَمۡوَٰلِكُمۡۚ إِنَّهُۥ كَانَ حُوبٗا كَبِيرٗا ﴾
[النِّسَاء: 2]

Apatseni ana a masiye chuma chawo akafika msinkhu woyenera. Musasinthitse choipa ndi chabwino ndipo musadye chuma chawo pamodzi ndi chanu chifukwa kutero, ndithudi, ndi tchimo lalikulu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وآتوا اليتامى أموالهم ولا تتبدلوا الخبيث بالطيب ولا تأكلوا أموالهم إلى أموالكم, باللغة نيانجا

﴿وآتوا اليتامى أموالهم ولا تتبدلوا الخبيث بالطيب ولا تأكلوا أموالهم إلى أموالكم﴾ [النِّسَاء: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo apatseni ana amasiye chuma chawo; musasinthanitse choipa ndi chabwino. Ndipo musadye chuma chawo pochiphatikiza ndi chuma chanu. Ndithudi, (zonsezo) ndiuchimo waukulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek