×

oh inu anthu! Muopeni Ambuye wanu amene anakulengani inu kuchokera kwa munthu 4:1 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:1) ayat 1 in Chichewa

4:1 Surah An-Nisa’ ayat 1 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 1 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّاسُ ٱتَّقُواْ رَبَّكُمُ ٱلَّذِي خَلَقَكُم مِّن نَّفۡسٖ وَٰحِدَةٖ وَخَلَقَ مِنۡهَا زَوۡجَهَا وَبَثَّ مِنۡهُمَا رِجَالٗا كَثِيرٗا وَنِسَآءٗۚ وَٱتَّقُواْ ٱللَّهَ ٱلَّذِي تَسَآءَلُونَ بِهِۦ وَٱلۡأَرۡحَامَۚ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ عَلَيۡكُمۡ رَقِيبٗا ﴾
[النِّسَاء: 1]

oh inu anthu! Muopeni Ambuye wanu amene anakulengani inu kuchokera kwa munthu mmodzi ndipo kuchokera kwa munthu ameneyu, Iye analenga mkazi wake. Ndipo kudzera mwa iwo, Iye adadzadza dziko lonse lapansi ndi anthu amuna ndi akazi osawerengeka. Opani Mulungu, dzina limene mumadandaulirana wina ndi mnzake. Ndipo lemekezani chibale. Ndithudi Mulungu amakuyang’anirani nthawi zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الناس اتقوا ربكم الذي خلقكم من نفس واحدة وخلق منها زوجها, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الناس اتقوا ربكم الذي خلقكم من نفس واحدة وخلق منها زوجها﴾ [النِّسَاء: 1]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek