×

Koma ngati inu mufuna kusudzula mkazi ndi cholinga chokwatira mkazi wina ndipo 4:20 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:20) ayat 20 in Chichewa

4:20 Surah An-Nisa’ ayat 20 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 20 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿وَإِنۡ أَرَدتُّمُ ٱسۡتِبۡدَالَ زَوۡجٖ مَّكَانَ زَوۡجٖ وَءَاتَيۡتُمۡ إِحۡدَىٰهُنَّ قِنطَارٗا فَلَا تَأۡخُذُواْ مِنۡهُ شَيۡـًٔاۚ أَتَأۡخُذُونَهُۥ بُهۡتَٰنٗا وَإِثۡمٗا مُّبِينٗا ﴾
[النِّسَاء: 20]

Koma ngati inu mufuna kusudzula mkazi ndi cholinga chokwatira mkazi wina ndipo mutampatsa mmodzi mwa iwo chuma chochuluka, ngati mphatso ya ukwati, musatenge chilichonse mwa chumacho. Kodi inu mungakhale mopanda chilungamo ndikuwonetsa kuchimwa poyera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن أردتم استبدال زوج مكان زوج وآتيتم إحداهن قنطارا فلا تأخذوا منه, باللغة نيانجا

﴿وإن أردتم استبدال زوج مكان زوج وآتيتم إحداهن قنطارا فلا تأخذوا منه﴾ [النِّسَاء: 20]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati mufuna kusintha mkazi wina m’malo mwa wina (pokwatira wina kusiya wakale) pomwe mmodzi wa iwo (woyambayo) mudampatsa milumilu ya chuma, musatenge (kulanda) chilichonse. Kodi mungachitenge mwa chinyengo ndi uchimo woonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek