×

Kodi iwo akadataya chiyani ngati akadakhulupirira mwa Mulungu ndi tsiku la chiweruzo 4:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:39) ayat 39 in Chichewa

4:39 Surah An-Nisa’ ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 39 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَمَاذَا عَلَيۡهِمۡ لَوۡ ءَامَنُواْ بِٱللَّهِ وَٱلۡيَوۡمِ ٱلۡأٓخِرِ وَأَنفَقُواْ مِمَّا رَزَقَهُمُ ٱللَّهُۚ وَكَانَ ٱللَّهُ بِهِمۡ عَلِيمًا ﴾
[النِّسَاء: 39]

Kodi iwo akadataya chiyani ngati akadakhulupirira mwa Mulungu ndi tsiku la chiweruzo ndi kupereka muzinthu zimene Mulungu adawapatsa iwo kuti ziziwathandiza? Mulungu amawadziwa onse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وماذا عليهم لو آمنوا بالله واليوم الآخر وأنفقوا مما رزقهم الله وكان, باللغة نيانجا

﴿وماذا عليهم لو آمنوا بالله واليوم الآخر وأنفقوا مما رزقهم الله وكان﴾ [النِّسَاء: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi pakadakhala vuto lanji kwa iwo ngati akadakhulupirira Allah ndi tsiku lachimaliziro napereka zina mwa zomwe Allah wawapatsa? Ndipo Allah ali Wodziwa bwino za iwo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek