×

Ndithudi! Mulungu sapondereza malipiro ngakhale a kanthu kochepa, ndipo ngati muli zabwino 4:40 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:40) ayat 40 in Chichewa

4:40 Surah An-Nisa’ ayat 40 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 40 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿إِنَّ ٱللَّهَ لَا يَظۡلِمُ مِثۡقَالَ ذَرَّةٖۖ وَإِن تَكُ حَسَنَةٗ يُضَٰعِفۡهَا وَيُؤۡتِ مِن لَّدُنۡهُ أَجۡرًا عَظِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 40]

Ndithudi! Mulungu sapondereza malipiro ngakhale a kanthu kochepa, ndipo ngati muli zabwino Iye adzakaonjezera malipiro ake ndipo amapereka kuchokera kwa Iye malipiro ochuluka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الله لا يظلم مثقال ذرة وإن تك حسنة يضاعفها ويؤت من, باللغة نيانجا

﴿إن الله لا يظلم مثقال ذرة وإن تك حسنة يضاعفها ويؤت من﴾ [النِّسَاء: 40]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, Allah sachitira (anthu) zosalungama ngakhale kanthu kolemera ngati kanyelere; ngati kanthuko kali kabwino amakachulukitsa ndi kupereka malipiro aakulu kuchokera kwa Iye
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek