×

Kodi siunaone iwo amene adapatsidwa gawo la Buku la Mulungu? Iwo amakhulupirira 4:51 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:51) ayat 51 in Chichewa

4:51 Surah An-Nisa’ ayat 51 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 51 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿أَلَمۡ تَرَ إِلَى ٱلَّذِينَ أُوتُواْ نَصِيبٗا مِّنَ ٱلۡكِتَٰبِ يُؤۡمِنُونَ بِٱلۡجِبۡتِ وَٱلطَّٰغُوتِ وَيَقُولُونَ لِلَّذِينَ كَفَرُواْ هَٰٓؤُلَآءِ أَهۡدَىٰ مِنَ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ سَبِيلًا ﴾
[النِّسَاء: 51]

Kodi siunaone iwo amene adapatsidwa gawo la Buku la Mulungu? Iwo amakhulupirira mafano ndi milungu yabodza ndipo amawauza osakhulupilira kuti ndi otsogozedwa bwino kuposa anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألم تر إلى الذين أوتوا نصيبا من الكتاب يؤمنون بالجبت والطاغوت ويقولون, باللغة نيانجا

﴿ألم تر إلى الذين أوتوا نصيبا من الكتاب يؤمنون بالجبت والطاغوت ويقولون﴾ [النِّسَاء: 51]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi sukuwaona omwe apatsidwa gawo la nzeru zozindikira buku (la Allah)? Amakhulupirira mafano ndi asatana, ndipo akumati kwa amene sadakhulupirire: “Awa ali panjira yoongoka kwabasi kuposa okhulupirira (Asilamu).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek