Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 53 - النِّسَاء - Page - Juz 5
﴿أَمۡ لَهُمۡ نَصِيبٞ مِّنَ ٱلۡمُلۡكِ فَإِذٗا لَّا يُؤۡتُونَ ٱلنَّاسَ نَقِيرًا ﴾
[النِّسَاء: 53]
﴿أم لهم نصيب من الملك فإذا لا يؤتون الناس نقيرا﴾ [النِّسَاء: 53]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi ali ndi gawo la ufumu (wa Allah? Nchifukwa ninji akunyasidwa munthu wina akaninkhidwa utumiki)? Zikadatero ndiye kuti sakadawapatsa anthu ngakhale kochepa kwambiri monga khokho la tende |