×

Kodi kapena iwo amachitira kaduka anthu mu zinthu zabwino zimene Mulungu wawapatsa? 4:54 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:54) ayat 54 in Chichewa

4:54 Surah An-Nisa’ ayat 54 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 54 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿أَمۡ يَحۡسُدُونَ ٱلنَّاسَ عَلَىٰ مَآ ءَاتَىٰهُمُ ٱللَّهُ مِن فَضۡلِهِۦۖ فَقَدۡ ءَاتَيۡنَآ ءَالَ إِبۡرَٰهِيمَ ٱلۡكِتَٰبَ وَٱلۡحِكۡمَةَ وَءَاتَيۡنَٰهُم مُّلۡكًا عَظِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 54]

Kodi kapena iwo amachitira kaduka anthu mu zinthu zabwino zimene Mulungu wawapatsa? Ife tidawapatsa ana a Abrahamu Buku ndi luntha ndipo tidawapatsa Ufumu waukulu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أم يحسدون الناس على ما آتاهم الله من فضله فقد آتينا آل, باللغة نيانجا

﴿أم يحسدون الناس على ما آتاهم الله من فضله فقد آتينا آل﴾ [النِّسَاء: 54]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi akuchitira anthu dumbo pa zomwe Allah wawapatsa ndi ufulu wake? Choncho tidalipatsa banja la Ibrahim buku ndi nzeru. Ndipo tidawapatsa ufumu waukulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek