×

Ndithudi Mulungu ali kukulamulirani kuti mubwezere katundu amene mwasunga kwa eni ake 4:58 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:58) ayat 58 in Chichewa

4:58 Surah An-Nisa’ ayat 58 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 58 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿۞ إِنَّ ٱللَّهَ يَأۡمُرُكُمۡ أَن تُؤَدُّواْ ٱلۡأَمَٰنَٰتِ إِلَىٰٓ أَهۡلِهَا وَإِذَا حَكَمۡتُم بَيۡنَ ٱلنَّاسِ أَن تَحۡكُمُواْ بِٱلۡعَدۡلِۚ إِنَّ ٱللَّهَ نِعِمَّا يَعِظُكُم بِهِۦٓۗ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ سَمِيعَۢا بَصِيرٗا ﴾
[النِّسَاء: 58]

Ndithudi Mulungu ali kukulamulirani kuti mubwezere katundu amene mwasunga kwa eni ake ndipo ngati muweruza pakati pa anthu, weruzani mwachilungamo. Ndithudi chilangizo chimene Mulungu akukulangizani ndi chabwino kwambiri. Ndithudi Mulungu amamva nthawi zonse ndipo amaona zinthu zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الله يأمركم أن تؤدوا الأمانات إلى أهلها وإذا حكمتم بين الناس, باللغة نيانجا

﴿إن الله يأمركم أن تؤدوا الأمانات إلى أهلها وإذا حكمتم بين الناس﴾ [النِّسَاء: 58]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek