×

Kodi ndi chifukwa chiyani inu simukumenya nkhondo m’njira ya Mulungu pamene anthu 4:75 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:75) ayat 75 in Chichewa

4:75 Surah An-Nisa’ ayat 75 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 75 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَمَا لَكُمۡ لَا تُقَٰتِلُونَ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ وَٱلۡمُسۡتَضۡعَفِينَ مِنَ ٱلرِّجَالِ وَٱلنِّسَآءِ وَٱلۡوِلۡدَٰنِ ٱلَّذِينَ يَقُولُونَ رَبَّنَآ أَخۡرِجۡنَا مِنۡ هَٰذِهِ ٱلۡقَرۡيَةِ ٱلظَّالِمِ أَهۡلُهَا وَٱجۡعَل لَّنَا مِن لَّدُنكَ وَلِيّٗا وَٱجۡعَل لَّنَا مِن لَّدُنكَ نَصِيرًا ﴾
[النِّسَاء: 75]

Kodi ndi chifukwa chiyani inu simukumenya nkhondo m’njira ya Mulungu pamene anthu ofoka mwa anthu amuna, akazi ndi ana amati: “Ambuye wathu! Tipulumutseni kuchoka kumzinda uwu wa anthu wochita zoipa ndipo tidzutsireni mtetezi wochokera kwa Inu amene adzatithandiza ife.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما لكم لا تقاتلون في سبيل الله والمستضعفين من الرجال والنساء والولدان, باللغة نيانجا

﴿وما لكم لا تقاتلون في سبيل الله والمستضعفين من الرجال والنساء والولدان﴾ [النِّسَاء: 75]

Khaled Ibrahim Betala
“Mwatani inu osamenyana pa njira ya Allah, ndi (kuwapulumutsa) omwe ali ofooka, aamuna ndi aakazi ndi ana, omwe akunena: “Mbuye wathu! Titulutseni m’mudzi uwu omwe anthu ake ndiopondereza; ndipo tipatseni mtetezi wochokera kwa Inu; ndiponso tipatseni mthandizi wochokera kwa Inu.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek