×

Iwo amati: “Ife ndife omvera” koma iwo akangochoka kwa iwe, ambiri a 4:81 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:81) ayat 81 in Chichewa

4:81 Surah An-Nisa’ ayat 81 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 81 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَيَقُولُونَ طَاعَةٞ فَإِذَا بَرَزُواْ مِنۡ عِندِكَ بَيَّتَ طَآئِفَةٞ مِّنۡهُمۡ غَيۡرَ ٱلَّذِي تَقُولُۖ وَٱللَّهُ يَكۡتُبُ مَا يُبَيِّتُونَۖ فَأَعۡرِضۡ عَنۡهُمۡ وَتَوَكَّلۡ عَلَى ٱللَّهِۚ وَكَفَىٰ بِٱللَّهِ وَكِيلًا ﴾
[النِّسَاء: 81]

Iwo amati: “Ife ndife omvera” koma iwo akangochoka kwa iwe, ambiri a iwo amachita chiwembu usiku pochita zinthu zimene siukunena. Koma Mulungu amalemba ziwembu zawo zonse zomwe amachita usiku. Kotero aleke okha ndipo ika chikhulupiliro chako mwa Mulungu. Ndipo Mulungu ndi okwana kukhala Mtetezi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويقولون طاعة فإذا برزوا من عندك بيت طائفة منهم غير الذي تقول, باللغة نيانجا

﴿ويقولون طاعة فإذا برزوا من عندك بيت طائفة منهم غير الذي تقول﴾ [النِّسَاء: 81]

Khaled Ibrahim Betala
“Amati: “Tikumvera.” Koma akachoka kwa iwe, gulu lina la iwo limapangana usiku zosagwirizana ndi zomwe ukunena (pamaso pawo). Koma Allah akulemba zonse zomwe akupangana. Choncho apatukire ndipo yadzamira kwa Allah. Ndipo Allah wakwanira kukhala Mtetezi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek