Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 13 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿هُوَ ٱلَّذِي يُرِيكُمۡ ءَايَٰتِهِۦ وَيُنَزِّلُ لَكُم مِّنَ ٱلسَّمَآءِ رِزۡقٗاۚ وَمَا يَتَذَكَّرُ إِلَّا مَن يُنِيبُ ﴾
[غَافِر: 13]
﴿هو الذي يريكم آياته وينـزل لكم من السماء رزقا وما يتذكر إلا﴾ [غَافِر: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Iye ndi Yemwe akukuonetsani zisonyezo Zake (zosonyeza mphamvu Yake yoposa), ndipo akukutsitsirani madzi kumwamba chifukwa cha inu kuti abweretse zokupatsani moyo (monga chakudya ndi zina). Koma palibe amene akukumbukira kwenikweni kupatula amene watembenukira (kwa Allah) |