×

Wokweza maudindo anthu okhulupirira ndi Mwini Mpando wachifumu. Iye amatumiza chikumbutso chake 40:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ghafir ⮕ (40:15) ayat 15 in Chichewa

40:15 Surah Ghafir ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 15 - غَافِر - Page - Juz 24

﴿رَفِيعُ ٱلدَّرَجَٰتِ ذُو ٱلۡعَرۡشِ يُلۡقِي ٱلرُّوحَ مِنۡ أَمۡرِهِۦ عَلَىٰ مَن يَشَآءُ مِنۡ عِبَادِهِۦ لِيُنذِرَ يَوۡمَ ٱلتَّلَاقِ ﴾
[غَافِر: 15]

Wokweza maudindo anthu okhulupirira ndi Mwini Mpando wachifumu. Iye amatumiza chikumbutso chake kwa aliyense wa akapolo ake amene Iye wamufuna kuti akhoza kuchenjeza anthu za tsiku lachiweruzo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: رفيع الدرجات ذو العرش يلقي الروح من أمره على من يشاء من, باللغة نيانجا

﴿رفيع الدرجات ذو العرش يلقي الروح من أمره على من يشاء من﴾ [غَافِر: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Iye Ngotukuka ulemelero, Mwini Arsh (Mpando wachifumu); amapereka chivumbulutso (Chake) mwa lamulo lake kwa yemwe wamfuna mwa akapolo Ake kuti achenjeze (anthu za) tsiku lokumana (anthu onse)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek