×

Tsiku limeneli, mzimu uliwonse udzalandira malipiro ake. Pa tsiku limeneli sikudzakhala kuponderezana. 40:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ghafir ⮕ (40:17) ayat 17 in Chichewa

40:17 Surah Ghafir ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 17 - غَافِر - Page - Juz 24

﴿ٱلۡيَوۡمَ تُجۡزَىٰ كُلُّ نَفۡسِۭ بِمَا كَسَبَتۡۚ لَا ظُلۡمَ ٱلۡيَوۡمَۚ إِنَّ ٱللَّهَ سَرِيعُ ٱلۡحِسَابِ ﴾
[غَافِر: 17]

Tsiku limeneli, mzimu uliwonse udzalandira malipiro ake. Pa tsiku limeneli sikudzakhala kuponderezana. Ndithudi Mulungu ndi wachangu pobwezera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: اليوم تجزى كل نفس بما كسبت لا ظلم اليوم إن الله سريع, باللغة نيانجا

﴿اليوم تجزى كل نفس بما كسبت لا ظلم اليوم إن الله سريع﴾ [غَافِر: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Mzimu uliwonse lero, ulipidwa zimene udachita; palibe kupondereza lero (pochepetsa mphoto kapena kuonjeza chilango). Ndithu Allah Ngwachangu (pa) chiwerengero Chake
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek