Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 65 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿هُوَ ٱلۡحَيُّ لَآ إِلَٰهَ إِلَّا هُوَ فَٱدۡعُوهُ مُخۡلِصِينَ لَهُ ٱلدِّينَۗ ٱلۡحَمۡدُ لِلَّهِ رَبِّ ٱلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[غَافِر: 65]
﴿هو الحي لا إله إلا هو فادعوه مخلصين له الدين الحمد لله﴾ [غَافِر: 65]
Khaled Ibrahim Betala “Iye Ngwamoyo Wamuyaya; palibe wopembedzedwa wina, koma Iye. Choncho mpembedzeni momuyeretsera chipembedzo. (Musapembedze milungu ina mophatikiza ndi Iye). Kuyamikidwa konse nkwa Allah, Mbuye wa zolengedwa |