×

Ichi ndi chifukwa chakuti inu munali kusangalala ndi zinthu zachabechabe padziko ndipo 40:75 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ghafir ⮕ (40:75) ayat 75 in Chichewa

40:75 Surah Ghafir ayat 75 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 75 - غَافِر - Page - Juz 24

﴿ذَٰلِكُم بِمَا كُنتُمۡ تَفۡرَحُونَ فِي ٱلۡأَرۡضِ بِغَيۡرِ ٱلۡحَقِّ وَبِمَا كُنتُمۡ تَمۡرَحُونَ ﴾
[غَافِر: 75]

Ichi ndi chifukwa chakuti inu munali kusangalala ndi zinthu zachabechabe padziko ndipo munali ndi mwano

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ذلكم بما كنتم تفرحون في الأرض بغير الحق وبما كنتم تمرحون, باللغة نيانجا

﴿ذلكم بما كنتم تفرحون في الأرض بغير الحق وبما كنتم تمرحون﴾ [غَافِر: 75]

Khaled Ibrahim Betala
““Izi, (zimene zakupezani ku Moto kuno), nchifukwa chakuti mudali kudzikweza pa dziko mosayenera. Ndiponso chifukwa chakuti mudali kunyada
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek