Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 10 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿وَجَعَلَ فِيهَا رَوَٰسِيَ مِن فَوۡقِهَا وَبَٰرَكَ فِيهَا وَقَدَّرَ فِيهَآ أَقۡوَٰتَهَا فِيٓ أَرۡبَعَةِ أَيَّامٖ سَوَآءٗ لِّلسَّآئِلِينَ ﴾
[فُصِّلَت: 10]
﴿وجعل فيها رواسي من فوقها وبارك فيها وقدر فيها أقواتها في أربعة﴾ [فُصِّلَت: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adaika pamenepo mapiri ataliatali pamwamba pake, ndi kudalitsapo (ndi madzi, mmera, ndi ziweto), ndipo adayesa mmenemo zakudya zake (za okhala pa nthakapo; zimenezi adadzichita) mmasiku anayi; (izi) nzokwanira kwa ofunsa (zakalengedwe ka nthaka ndi zamkati mwake) |