Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 11 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿ثُمَّ ٱسۡتَوَىٰٓ إِلَى ٱلسَّمَآءِ وَهِيَ دُخَانٞ فَقَالَ لَهَا وَلِلۡأَرۡضِ ٱئۡتِيَا طَوۡعًا أَوۡ كَرۡهٗا قَالَتَآ أَتَيۡنَا طَآئِعِينَ ﴾
[فُصِّلَت: 11]
﴿ثم استوى إلى السماء وهي دخان فقال لها وللأرض ائتيا طوعا أو﴾ [فُصِّلَت: 11]
Khaled Ibrahim Betala “Kenako adalunjika ku thambo (malunjikidwe ogwirizana ndimomwe Iye alili mosafanana ndi zolengedwa zake), pomwe ilo (thambolo) lidali utsi. Ndipo adati kwa ilo ndi nthaka: “Idzani, mofuna kapena mokakamizidwa (tsatirani lamulo Langa).” Izo zidayankha kuti: “Tadza mofuna.” |