×

Nena, “Kodi, ndithudi, inu muli kumukana Iye amene adalenga dziko lapansi m’masiku 41:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:9) ayat 9 in Chichewa

41:9 Surah Fussilat ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 9 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿۞ قُلۡ أَئِنَّكُمۡ لَتَكۡفُرُونَ بِٱلَّذِي خَلَقَ ٱلۡأَرۡضَ فِي يَوۡمَيۡنِ وَتَجۡعَلُونَ لَهُۥٓ أَندَادٗاۚ ذَٰلِكَ رَبُّ ٱلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[فُصِّلَت: 9]

Nena, “Kodi, ndithudi, inu muli kumukana Iye amene adalenga dziko lapansi m’masiku awiri ndipo muli kumufanizirandienakukhalaofanananaye? IyendiAmbuye wa zolengedwa zonse.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل أئنكم لتكفرون بالذي خلق الأرض في يومين وتجعلون له أندادا ذلك, باللغة نيانجا

﴿قل أئنكم لتكفرون بالذي خلق الأرض في يومين وتجعلون له أندادا ذلك﴾ [فُصِّلَت: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Kodi inu mukumkanira yemwe adalenga nthaka mmasiku awiri (okha)? Ndipo mukumpangira milungu (ina)? Iyeyo ndiye Mbuye wa zolengedwa zonse.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek