Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 36 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿وَإِمَّا يَنزَغَنَّكَ مِنَ ٱلشَّيۡطَٰنِ نَزۡغٞ فَٱسۡتَعِذۡ بِٱللَّهِۖ إِنَّهُۥ هُوَ ٱلسَّمِيعُ ٱلۡعَلِيمُ ﴾
[فُصِّلَت: 36]
﴿وإما ينـزغنك من الشيطان نـزغ فاستعذ بالله إنه هو السميع العليم﴾ [فُصِّلَت: 36]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati satana atakusokoneza kuti akuchotse ku zomwe walamulidwa, pempha chitetezo kwa Allah. Ndithu Iye Ngwakumva zonse, Ngodziwa zonse; (adzakuteteza kwa iye) |