×

Ndipo pakati pa zizindikiro zake pali usiku ndi usana ndiponso dzuwa ndi 41:37 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:37) ayat 37 in Chichewa

41:37 Surah Fussilat ayat 37 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 37 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿وَمِنۡ ءَايَٰتِهِ ٱلَّيۡلُ وَٱلنَّهَارُ وَٱلشَّمۡسُ وَٱلۡقَمَرُۚ لَا تَسۡجُدُواْ لِلشَّمۡسِ وَلَا لِلۡقَمَرِ وَٱسۡجُدُواْۤ لِلَّهِۤ ٱلَّذِي خَلَقَهُنَّ إِن كُنتُمۡ إِيَّاهُ تَعۡبُدُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 37]

Ndipo pakati pa zizindikiro zake pali usiku ndi usana ndiponso dzuwa ndi mwezi. Musagwadire dzuwa kapena mwezi koma mugwadire Mulungu amene adazilenga izo ngati ndiye amene inu mumamupembedza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن آياته الليل والنهار والشمس والقمر لا تسجدوا للشمس ولا للقمر واسجدوا, باللغة نيانجا

﴿ومن آياته الليل والنهار والشمس والقمر لا تسجدوا للشمس ولا للقمر واسجدوا﴾ [فُصِّلَت: 37]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo zina mwa zisonyezo Zake, ndi usiku, usana, dzuwa ndi mwezi. Musalambire dzuwa ngakhale mwezi, koma lambirani Allah, Amene adazilenga ngati inu mukumpembedza mwachoonadi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek