Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 35 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿وَمَا يُلَقَّىٰهَآ إِلَّا ٱلَّذِينَ صَبَرُواْ وَمَا يُلَقَّىٰهَآ إِلَّا ذُو حَظٍّ عَظِيمٖ ﴾
[فُصِّلَت: 35]
﴿وما يلقاها إلا الذين صبروا وما يلقاها إلا ذو حظ عظيم﴾ [فُصِّلَت: 35]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo palibe angapatsidwe zimenezi (zochotsa choipa pochita chabwino) kupatula amene apirira. Ndiponso sangapatsidwe zimenezi kupatula mwini gawo la ubwino waukulu |