×

Ndipo pakati pa zizindikiro zake pali choti inu mumaona nthaka ili youma 41:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:39) ayat 39 in Chichewa

41:39 Surah Fussilat ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 39 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿وَمِنۡ ءَايَٰتِهِۦٓ أَنَّكَ تَرَى ٱلۡأَرۡضَ خَٰشِعَةٗ فَإِذَآ أَنزَلۡنَا عَلَيۡهَا ٱلۡمَآءَ ٱهۡتَزَّتۡ وَرَبَتۡۚ إِنَّ ٱلَّذِيٓ أَحۡيَاهَا لَمُحۡيِ ٱلۡمَوۡتَىٰٓۚ إِنَّهُۥ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٌ ﴾
[فُصِّلَت: 39]

Ndipo pakati pa zizindikiro zake pali choti inu mumaona nthaka ili youma koma pamene Ife titumiza pa nthakayo madzi, iyo imakhala ndi moyo ndipo imakhala ndi zomera zambiri. Ndithudi, Iye amapereka moyo ku nthaka youma, ndithudi, akhoza kuperekanso moyo kwa anthu amene adafa. Ndithudi Iye ali ndi mphamvu pa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن آياته أنك ترى الأرض خاشعة فإذا أنـزلنا عليها الماء اهتزت وربت, باللغة نيانجا

﴿ومن آياته أنك ترى الأرض خاشعة فإذا أنـزلنا عليها الماء اهتزت وربت﴾ [فُصِّلَت: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo zina mwa zisonyezo Zake (zoposa), ndithu iwe umaona nthaka ili youma; koma tikatsitsa madzi pa iyo imagwedezeka ndi kufufuma; ndithu Amene waiukitsa nthaka itauma, Ngoukitsa akufa. Iye Ngwamphamvu zoposa pa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek