Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 38 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿فَإِنِ ٱسۡتَكۡبَرُواْ فَٱلَّذِينَ عِندَ رَبِّكَ يُسَبِّحُونَ لَهُۥ بِٱلَّيۡلِ وَٱلنَّهَارِ وَهُمۡ لَا يَسۡـَٔمُونَ۩ ﴾
[فُصِّلَت: 38]
﴿فإن استكبروا فالذين عند ربك يسبحون له بالليل والنهار وهم لا يسأمون﴾ [فُصِّلَت: 38]
Khaled Ibrahim Betala “Koma ngati adzikweza (opembedza mafano ndi kusiya kutsatira lamulo lako, usade nkhawa). Ndipo, amene ali kwa Mbuye wako; (angelo), akulemekeza Iye usiku ndi usana, ndipo iwo satopa (ndi kutamanda Allah) |