Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 40 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ يُلۡحِدُونَ فِيٓ ءَايَٰتِنَا لَا يَخۡفَوۡنَ عَلَيۡنَآۗ أَفَمَن يُلۡقَىٰ فِي ٱلنَّارِ خَيۡرٌ أَم مَّن يَأۡتِيٓ ءَامِنٗا يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِۚ ٱعۡمَلُواْ مَا شِئۡتُمۡ إِنَّهُۥ بِمَا تَعۡمَلُونَ بَصِيرٌ ﴾
[فُصِّلَت: 40]
﴿إن الذين يلحدون في آياتنا لا يخفون علينا أفمن يلقى في النار﴾ [فُصِّلَت: 40]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu amene akupotoza choonadi mzisonyezo Zathu sangabisike kwa Ife. (Ndipo tidzawalipira zimene akuyenerana nazo). Kodi wabwino ndi uti, yemwe adzaponyedwa ku Moto, kapena yemwe adzadza pa tsiku la chiweruziro uku ali wokhazikika mtima? Chitani zimene mukufuna; ndithu Iye Ngopenya chilichonse chimene mukuchita. (Aliyense adzamulipira pa zochita zake) |