Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 29 - الشُّوري - Page - Juz 25
﴿وَمِنۡ ءَايَٰتِهِۦ خَلۡقُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَمَا بَثَّ فِيهِمَا مِن دَآبَّةٖۚ وَهُوَ عَلَىٰ جَمۡعِهِمۡ إِذَا يَشَآءُ قَدِيرٞ ﴾
[الشُّوري: 29]
﴿ومن آياته خلق السموات والأرض وما بث فيهما من دابة وهو على﴾ [الشُّوري: 29]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo zina mwa zisonyezo zake ndi kulenga kwa thambo ndi nthaka, ndi zamoyo zimene wazifalitsa mmenemo (zooneka ndi zosaoneka). Ndipo Iye ndi Wamphamvu zowasonkhanitsira (anthu kuchokera ku imfa) akadzafuna |