×

Ndipo inu simungathe kuthawa padziko lapansi ndipo inu mulibe wina aliyense kupatula 42:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ash-Shura ⮕ (42:31) ayat 31 in Chichewa

42:31 Surah Ash-Shura ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 31 - الشُّوري - Page - Juz 25

﴿وَمَآ أَنتُم بِمُعۡجِزِينَ فِي ٱلۡأَرۡضِۖ وَمَا لَكُم مِّن دُونِ ٱللَّهِ مِن وَلِيّٖ وَلَا نَصِيرٖ ﴾
[الشُّوري: 31]

Ndipo inu simungathe kuthawa padziko lapansi ndipo inu mulibe wina aliyense kupatula Mulungu amene angakutetezeni kapena kukuthandizani

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما أنتم بمعجزين في الأرض وما لكم من دون الله من ولي, باللغة نيانجا

﴿وما أنتم بمعجزين في الأرض وما لكم من دون الله من ولي﴾ [الشُّوري: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo simungathe kum’lepheretsa (Allah kukutsitsirani mavuto) padziko lapansi (ngati mutachimwa); ndipo inu mulibenso mthandizi kapena mpulumutsi kupatula Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek