×

Ndi iwo amene amapewa kuchita machimo aakuluakulu ndi zinthu zochititsa manyazi ndipo 42:37 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ash-Shura ⮕ (42:37) ayat 37 in Chichewa

42:37 Surah Ash-Shura ayat 37 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 37 - الشُّوري - Page - Juz 25

﴿وَٱلَّذِينَ يَجۡتَنِبُونَ كَبَٰٓئِرَ ٱلۡإِثۡمِ وَٱلۡفَوَٰحِشَ وَإِذَا مَا غَضِبُواْ هُمۡ يَغۡفِرُونَ ﴾
[الشُّوري: 37]

Ndi iwo amene amapewa kuchita machimo aakuluakulu ndi zinthu zochititsa manyazi ndipo pamene akwiya amakhululuka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين يجتنبون كبائر الإثم والفواحش وإذا ما غضبوا هم يغفرون, باللغة نيانجا

﴿والذين يجتنبون كبائر الإثم والفواحش وإذا ما غضبوا هم يغفرون﴾ [الشُّوري: 37]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akupewa machimo akuluakulu omwe Allah waletsa ndi machimo onse oipitsitsa; ndipo iwo akakwiya (chifukwa choputidwa) iwo amakhululuka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek