Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 49 - الشُّوري - Page - Juz 25
﴿لِّلَّهِ مُلۡكُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۚ يَخۡلُقُ مَا يَشَآءُۚ يَهَبُ لِمَن يَشَآءُ إِنَٰثٗا وَيَهَبُ لِمَن يَشَآءُ ٱلذُّكُورَ ﴾
[الشُّوري: 49]
﴿لله ملك السموات والأرض يخلق ما يشاء يهب لمن يشاء إناثا ويهب﴾ [الشُّوري: 49]
Khaled Ibrahim Betala “Ufumu wakumwamba ndi pa dziko lapansi ngwa Allah; amalenga zimene wafuna; amene wam’funa amampatsa ana achikazi (okhaokha) ndiponso amene wamfuna amampatsa ana achimuna (okhaokha) |