×

Ndipo ndiye amene amatumiza mvula kuchokera kumitambo molingana ndi muyeso. Ndipo Ife 43:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zukhruf ⮕ (43:11) ayat 11 in Chichewa

43:11 Surah Az-Zukhruf ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 11 - الزُّخرُف - Page - Juz 25

﴿وَٱلَّذِي نَزَّلَ مِنَ ٱلسَّمَآءِ مَآءَۢ بِقَدَرٖ فَأَنشَرۡنَا بِهِۦ بَلۡدَةٗ مَّيۡتٗاۚ كَذَٰلِكَ تُخۡرَجُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 11]

Ndipo ndiye amene amatumiza mvula kuchokera kumitambo molingana ndi muyeso. Ndipo Ife timadzutsa nthaka imene idali yakufa ndi iyo, kotero nanunso mudzadzutsidwa chimodzimodzi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذي نـزل من السماء ماء بقدر فأنشرنا به بلدة ميتا كذلك تخرجون, باللغة نيانجا

﴿والذي نـزل من السماء ماء بقدر فأنشرنا به بلدة ميتا كذلك تخرجون﴾ [الزُّخرُف: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndiponso amene watsitsa madzi kuchokera kumwamba mwamuyeso; chifukwa cha madziwo tidaukitsa mudzi wakufa. Momwemonso inu mudzatulutsidwa (mmanda)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek