Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 44 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَإِنَّهُۥ لَذِكۡرٞ لَّكَ وَلِقَوۡمِكَۖ وَسَوۡفَ تُسۡـَٔلُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 44]
﴿وإنه لذكر لك ولقومك وسوف تسألون﴾ [الزُّخرُف: 44]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu iyi (Qur’an) ndi ulemelero wako ndi anthu ako; ndipo posachedwa mufunsidwa (za ulemelero umenewu) |