Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 77 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَنَادَوۡاْ يَٰمَٰلِكُ لِيَقۡضِ عَلَيۡنَا رَبُّكَۖ قَالَ إِنَّكُم مَّٰكِثُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 77]
﴿ونادوا يامالك ليقض علينا ربك قال إنكم ماكثون﴾ [الزُّخرُف: 77]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (okanira) adzaitana E iwe Malik! (yemwe ndi mngelo woyang’anira moto): ‘‘Mbuye wako atipatse imfa (kuti tipumule kuchilangochi!)” Adzanena (Malik): “Ndithu inu mukhala momwemo!” |