Quran with Chichewa translation - Surah Ad-Dukhan ayat 4 - الدُّخان - Page - Juz 25
﴿فِيهَا يُفۡرَقُ كُلُّ أَمۡرٍ حَكِيمٍ ﴾
[الدُّخان: 4]
﴿فيها يفرق كل أمر حكيم﴾ [الدُّخان: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Mu (usiku) umenewu chinthu chilichonse chanzeru chimaweruzidwa ndi kulongosoledwa |