×

Kutsogolo kwawo kuli Gahena, ndipo sadzapeza phindu lina lililonse pa ntchito zawo 45:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:10) ayat 10 in Chichewa

45:10 Surah Al-Jathiyah ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 10 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿مِّن وَرَآئِهِمۡ جَهَنَّمُۖ وَلَا يُغۡنِي عَنۡهُم مَّا كَسَبُواْ شَيۡـٔٗا وَلَا مَا ٱتَّخَذُواْ مِن دُونِ ٱللَّهِ أَوۡلِيَآءَۖ وَلَهُمۡ عَذَابٌ عَظِيمٌ ﴾
[الجاثِية: 10]

Kutsogolo kwawo kuli Gahena, ndipo sadzapeza phindu lina lililonse pa ntchito zawo kapenakwaiwoameneadawasandutsakukhalawowasamala poonjezera pa Mulungu. Ndipo iwo adzalandira chilango chowawa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: من ورائهم جهنم ولا يغني عنهم ما كسبوا شيئا ولا ما اتخذوا, باللغة نيانجا

﴿من ورائهم جهنم ولا يغني عنهم ما كسبوا شيئا ولا ما اتخذوا﴾ [الجاثِية: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Jahannam ili (kuwayembekezera) kuseri kwawo; ndipo zimene adachita sizidzawathandiza chilichonse, ngakhale atetezi amene adadzipangira kusiya Allah (sadzawathandiza); ndipo adzapeza chilango chachikulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek