×

Ndipoiwe udzaona mtundu uliwonse utagwada pansi ndipo mtundu uliwonse udzaitanidwa monga mmene 45:28 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:28) ayat 28 in Chichewa

45:28 Surah Al-Jathiyah ayat 28 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 28 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿وَتَرَىٰ كُلَّ أُمَّةٖ جَاثِيَةٗۚ كُلُّ أُمَّةٖ تُدۡعَىٰٓ إِلَىٰ كِتَٰبِهَا ٱلۡيَوۡمَ تُجۡزَوۡنَ مَا كُنتُمۡ تَعۡمَلُونَ ﴾
[الجاثِية: 28]

Ndipoiwe udzaona mtundu uliwonse utagwada pansi ndipo mtundu uliwonse udzaitanidwa monga mmene zidalembedwera. Lero mudzalipidwa molingana ndi zimene mudachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وترى كل أمة جاثية كل أمة تدعى إلى كتابها اليوم تجزون ما, باللغة نيانجا

﴿وترى كل أمة جاثية كل أمة تدعى إلى كتابها اليوم تجزون ما﴾ [الجاثِية: 28]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo udzaliona gulu lililonse litagwada (uku nkhope zili zyoli); gulu lililonse lidzaitanidwa ku kaundula wake (kukamuwerenga): “Lero mulipidwa zimene mudali kuchita!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek