×

Kumvera ndi mau abwino (zikadakhala zinthu zabwino). Ndipo pamene nkhani iweruzidwa, ndipo 47:21 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Muhammad ⮕ (47:21) ayat 21 in Chichewa

47:21 Surah Muhammad ayat 21 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 21 - مُحمد - Page - Juz 26

﴿طَاعَةٞ وَقَوۡلٞ مَّعۡرُوفٞۚ فَإِذَا عَزَمَ ٱلۡأَمۡرُ فَلَوۡ صَدَقُواْ ٱللَّهَ لَكَانَ خَيۡرٗا لَّهُمۡ ﴾
[مُحمد: 21]

Kumvera ndi mau abwino (zikadakhala zinthu zabwino). Ndipo pamene nkhani iweruzidwa, ndipo iwo akadadzipereka mwachoonadi kwa Mulungu, ndithudi, zikadakhala zabwino kwa iwo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: طاعة وقول معروف فإذا عزم الأمر فلو صدقوا الله لكان خيرا لهم, باللغة نيانجا

﴿طاعة وقول معروف فإذا عزم الأمر فلو صدقوا الله لكان خيرا لهم﴾ [مُحمد: 21]

Khaled Ibrahim Betala
“(Zofunika ndi) kumvera ndi mawu abwino ndi kuti chinthu chikatsimikizika (achichite). Ngati akadamumvera Allah, ndithu zikadakhala zabwino kwa iwo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek