×

Ichi ndi chifukwa chakuti iwo amatsatira zinthu zimene zimakwiyitsa Mulungu ndipo amadana 47:28 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Muhammad ⮕ (47:28) ayat 28 in Chichewa

47:28 Surah Muhammad ayat 28 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 28 - مُحمد - Page - Juz 26

﴿ذَٰلِكَ بِأَنَّهُمُ ٱتَّبَعُواْ مَآ أَسۡخَطَ ٱللَّهَ وَكَرِهُواْ رِضۡوَٰنَهُۥ فَأَحۡبَطَ أَعۡمَٰلَهُمۡ ﴾
[مُحمد: 28]

Ichi ndi chifukwa chakuti iwo amatsatira zinthu zimene zimakwiyitsa Mulungu ndipo amadana ndi zimene zimamukondweretsa Iye. Kotero Mulungu adasandutsa ntchito zawo kukhala zinthu zopanda pake

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ذلك بأنهم اتبعوا ما أسخط الله وكرهوا رضوانه فأحبط أعمالهم, باللغة نيانجا

﴿ذلك بأنهم اتبعوا ما أسخط الله وكرهوا رضوانه فأحبط أعمالهم﴾ [مُحمد: 28]

Khaled Ibrahim Betala
“Zimenezi (imfa yoopsayi) nkaamba kakuti iwo adatsata zomwe zidakwiitsa Allah ndi kuda zomusangalatsa (Allah); choncho adaziwononga zochita zawo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek