×

Ndithudi onse amene sakhulupirira ndipo amaletsa anthu kutsatira njira ya Mulungu, ndipo 47:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Muhammad ⮕ (47:34) ayat 34 in Chichewa

47:34 Surah Muhammad ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 34 - مُحمد - Page - Juz 26

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ وَصَدُّواْ عَن سَبِيلِ ٱللَّهِ ثُمَّ مَاتُواْ وَهُمۡ كُفَّارٞ فَلَن يَغۡفِرَ ٱللَّهُ لَهُمۡ ﴾
[مُحمد: 34]

Ndithudi onse amene sakhulupirira ndipo amaletsa anthu kutsatira njira ya Mulungu, ndipo amafa ali osakhulupirira Mulungu sadzawakhululukira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين كفروا وصدوا عن سبيل الله ثم ماتوا وهم كفار فلن, باللغة نيانجا

﴿إن الذين كفروا وصدوا عن سبيل الله ثم ماتوا وهم كفار فلن﴾ [مُحمد: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu amene sadakhulupirire ndi kwatsekereza anthu kunjira ya Allah, kenako nkufa uku ali osakhulupirira Allah sadzawakhululukira (zolakwa zawo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek