Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 37 - مُحمد - Page - Juz 26
﴿إِن يَسۡـَٔلۡكُمُوهَا فَيُحۡفِكُمۡ تَبۡخَلُواْ وَيُخۡرِجۡ أَضۡغَٰنَكُمۡ ﴾
[مُحمد: 37]
﴿إن يسألكموها فيحفكم تبخلوا ويخرج أضغانكم﴾ [مُحمد: 37]
Khaled Ibrahim Betala “Ngati akadachifuna (kuchokera) kwa inu chumacho ndi kukuchulukitsirani (chopereka),mukadachita umbombo (ndi chumacho), ndipo akadatulutsira (poyera) kaduka kanu |