×

Ngati magulu awiri ochokera kwa anthu okhulupirira amenyana, khazikitsa mtendere pakati pawo. 49:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hujurat ⮕ (49:9) ayat 9 in Chichewa

49:9 Surah Al-hujurat ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hujurat ayat 9 - الحُجُرَات - Page - Juz 26

﴿وَإِن طَآئِفَتَانِ مِنَ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ٱقۡتَتَلُواْ فَأَصۡلِحُواْ بَيۡنَهُمَاۖ فَإِنۢ بَغَتۡ إِحۡدَىٰهُمَا عَلَى ٱلۡأُخۡرَىٰ فَقَٰتِلُواْ ٱلَّتِي تَبۡغِي حَتَّىٰ تَفِيٓءَ إِلَىٰٓ أَمۡرِ ٱللَّهِۚ فَإِن فَآءَتۡ فَأَصۡلِحُواْ بَيۡنَهُمَا بِٱلۡعَدۡلِ وَأَقۡسِطُوٓاْۖ إِنَّ ٱللَّهَ يُحِبُّ ٱلۡمُقۡسِطِينَ ﴾
[الحُجُرَات: 9]

Ngati magulu awiri ochokera kwa anthu okhulupirira amenyana, khazikitsa mtendere pakati pawo. Koma ngati gulu lina liswa malamulo mopyola muyeso, nonse menyanani nalo gulu lotero mpaka pamene limvera lamulo la Mulungu. Ndipo ngati ilo limvera, khazikitsani mtendere pakati pawo mwachilungamo. Ndithudi Mulungu amakonda iwo amene amachita chilungamo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن طائفتان من المؤمنين اقتتلوا فأصلحوا بينهما فإن بغت إحداهما على الأخرى, باللغة نيانجا

﴿وإن طائفتان من المؤمنين اقتتلوا فأصلحوا بينهما فإن بغت إحداهما على الأخرى﴾ [الحُجُرَات: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati magulu awiri aokhulupirira atamenyana ayanjanitseni pakati pawo. Ngati gulu limodzi mwa magulu awiriwo likuchitira mtopola linalo, limenyeni limene likuchita mtopola mpaka libwelere ku lamulo la Allah; ngati litabwerera, ayanjanitseni pakati pawo mwachilungamo, ndipo chitani chilungamo; ndithu Allah amakonda ochita chilungamo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek