Quran with Chichewa translation - Surah Al-hujurat ayat 8 - الحُجُرَات - Page - Juz 26
﴿فَضۡلٗا مِّنَ ٱللَّهِ وَنِعۡمَةٗۚ وَٱللَّهُ عَلِيمٌ حَكِيمٞ ﴾
[الحُجُرَات: 8]
﴿فضلا من الله ونعمة والله عليم حكيم﴾ [الحُجُرَات: 8]
Khaled Ibrahim Betala “(Chifukwa cha) ubwino wochokera kwa Allah ndi mtendere (Wake, mwapeza zimenezi); ndipo Allah Ngodziwa, Ngwanzeru zakuya |