Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 109 - المَائدة - Page - Juz 7
﴿۞ يَوۡمَ يَجۡمَعُ ٱللَّهُ ٱلرُّسُلَ فَيَقُولُ مَاذَآ أُجِبۡتُمۡۖ قَالُواْ لَا عِلۡمَ لَنَآۖ إِنَّكَ أَنتَ عَلَّٰمُ ٱلۡغُيُوبِ ﴾
[المَائدة: 109]
﴿يوم يجمع الله الرسل فيقول ماذا أجبتم قالوا لا علم لنا إنك﴾ [المَائدة: 109]
Khaled Ibrahim Betala “(Kumbukirani) tsiku lomwe Allah adzasonkhanitsa, atumiki ndikuwafunsa kuti: “Kodi mudayankhidwa chiyani?” Iwo adzati: “Ife sitidziwa. Ndithudi, Inuyo ndiye Wodziwa zamseri.” |