×

Iwo adati: “Ife tifuna kudya kuchokera pa ilo kuti mitima yathu ikhazikike 5:113 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:113) ayat 113 in Chichewa

5:113 Surah Al-Ma’idah ayat 113 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 113 - المَائدة - Page - Juz 7

﴿قَالُواْ نُرِيدُ أَن نَّأۡكُلَ مِنۡهَا وَتَطۡمَئِنَّ قُلُوبُنَا وَنَعۡلَمَ أَن قَدۡ صَدَقۡتَنَا وَنَكُونَ عَلَيۡهَا مِنَ ٱلشَّٰهِدِينَ ﴾
[المَائدة: 113]

Iwo adati: “Ife tifuna kudya kuchokera pa ilo kuti mitima yathu ikhazikike ndi kudziwa kuti zonse zimene udatiuza ife ndi zoona, ndipo kuti ife tikhoza kukhala mboni wa izo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا نريد أن نأكل منها وتطمئن قلوبنا ونعلم أن قد صدقتنا ونكون, باللغة نيانجا

﴿قالوا نريد أن نأكل منها وتطمئن قلوبنا ونعلم أن قد صدقتنا ونكون﴾ [المَائدة: 113]

Khaled Ibrahim Betala
“(Iwo) adati: “Tikufuna kudya chimenecho, ndikuti mitima yathu ikhazikike, ndikutinso tidziwe kuti watiuza choona; tero kuti tikhale oikira umboni pa chimenecho.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek