×

Anthu awiri amene amaopa ndiponso amene Mulungu adaonetsa chisomo chake adati: “Amenyeni 5:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:23) ayat 23 in Chichewa

5:23 Surah Al-Ma’idah ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 23 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿قَالَ رَجُلَانِ مِنَ ٱلَّذِينَ يَخَافُونَ أَنۡعَمَ ٱللَّهُ عَلَيۡهِمَا ٱدۡخُلُواْ عَلَيۡهِمُ ٱلۡبَابَ فَإِذَا دَخَلۡتُمُوهُ فَإِنَّكُمۡ غَٰلِبُونَۚ وَعَلَى ٱللَّهِ فَتَوَكَّلُوٓاْ إِن كُنتُم مُّؤۡمِنِينَ ﴾
[المَائدة: 23]

Anthu awiri amene amaopa ndiponso amene Mulungu adaonetsa chisomo chake adati: “Amenyeni kudzera pa chipata, chifukwa ngati inu mulowa, mudzapambana ndipo ikani chikhulupiliro chanu mwa Mulungu ngati inu ndinu wokhulupilira.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال رجلان من الذين يخافون أنعم الله عليهما ادخلوا عليهم الباب فإذا, باللغة نيانجا

﴿قال رجلان من الذين يخافون أنعم الله عليهما ادخلوا عليهم الباب فإذا﴾ [المَائدة: 23]

Khaled Ibrahim Betala
“Anthu awiri mwa amene ankaopa Allah, omwe awiriwo Allah adawapatsa chisomo, adati (kwa anzawo): “Alowereni pa chipata (cha dzikolo). Ngati mukalowamo ndithudi, inu mukapambana. Ndipo kwa Allah Yekha yadzamirani ngati inu mulidi okhulupirira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek