×

Koma aliyense amene alapa pambuyo pochimwa, ndipo achita ntchito zabwino, ndithu Mulungu 5:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:39) ayat 39 in Chichewa

5:39 Surah Al-Ma’idah ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 39 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿فَمَن تَابَ مِنۢ بَعۡدِ ظُلۡمِهِۦ وَأَصۡلَحَ فَإِنَّ ٱللَّهَ يَتُوبُ عَلَيۡهِۚ إِنَّ ٱللَّهَ غَفُورٞ رَّحِيمٌ ﴾
[المَائدة: 39]

Koma aliyense amene alapa pambuyo pochimwa, ndipo achita ntchito zabwino, ndithu Mulungu adzalandira kulapa kwake. Ndithudi Mulungu ndi okhululukira ndi wachisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فمن تاب من بعد ظلمه وأصلح فإن الله يتوب عليه إن الله, باللغة نيانجا

﴿فمن تاب من بعد ظلمه وأصلح فإن الله يتوب عليه إن الله﴾ [المَائدة: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma amene walapa pambuyo pakuchita kwake zoipa, namachita zabwino, Allah alandira kulapa kwake. Ndithudi, Allah Ngokhululuka kwabasi Ngwachisoni chosatha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek